1 Kings 20:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ahabu, mfumu ya ku Israele, adayankha kuti, “Monga m'mene mbuyanga mfumu akuneneramo, ineyo ndine wake pamodzi ndi zonse zomwe ndili nazo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu ya Israele anayankha, nati, Monga mwanena, mbuye wanga mfumu, ndine wanu ndi zonse ndili nazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu ya Israeli inayankha kuti, “Monga mmene mwanenera, mbuye wanga mfumu, ine pamodzi ndi zonse zomwe ndili nazo ndi zanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu ya Israyeli anayankha, nati, Monga mwanena, mbuye wanga mfumu, ndine wanu ndi zonse ndiri nazo.