1 Kings 20:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mneneriyo adamuuza kuti, “Chauta akunena kuti, ‘Poti wamtaya munthu amene Ine ndidati umuphe, ndiye kuti iweyo ndiwe amene udzaphedwe m'malo mwa iyeyo, ndipo anthu ako adzaphedwa m'malo mwa anthu ake.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Niti kwa iye, Atero Yehova, Popeza wataya m'dzanja lako munthu uja ndinati ndimuononge konse, moyo wako udzakhala m'malo mwa moyo wake, ndi anthu ako m'malo mwa anthu ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawuza mfumu kuti, “Yehova akuti, ‘Chifukwa chakuti mwamasula munthu amene Ine ndinati ndi woyenera kuphedwa, inuyo ndi amene mudzaphedwe mʼmalo mwa iyeyo, anthu anu mʼmalo mwa anthu ake.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Niti kwa iye, Atero Yehova, Popeza wataya m'dzanja lako munthu uja ndinati ndimuononge konse, moyo wako udzakhala m'malo mwamoyo wace, ndi anthu ako m'malo mwa anthu ace.