1 Kings 20:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Ahabu, mfumu ya ku Israele, adabwerera kunyumba kwake mwachisoni ndi mosakondwa, naloŵa mu mzinda wa Samariya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mfumu ya Israele inanka kwao wamsunamo ndi wokwiya, nafika ku Samariya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwachisoni ndi mokwiya, mfumu ya Israeli inapita ku nyumba yake yaufumu ku Samariya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mfumu ya Israyeli inamka kwao wamsunamo ndi wokwiya, nafika ku Samaria.