1 Kings 20:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuluakulu onsewo pamodzi ndi anthu omwe adati, “Musasamaleko zimenezo kapena kumuvomereza ai.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akulu onse ndi anthu onse anati kwa iye, Musamvere, musavomereze.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuluakulu onse ndi anthu onse anayankha kuti, “Musamumvere kapena kuvomereza zofuna zake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akulu onse ndi anthu onse anati kwa iye, Musamvere, musabvomereze.