1 Kings 21:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panali munthu wina wa ku Yezireele dzina lake Naboti. Iyeyo anali ndi munda wamphesa ku Yezireele, pafupi ndi nyumba ya mfumu Ahabu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zitatha izi, kunaoneka zotere: Naboti wa ku Yezireele anali ndi munda wamphesa, unali m'Yezireelemo, m'mbali mwa nyumba ya Ahabu mfumu ya ku Samariya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zitatha izi, panachitika nkhani yokhudza Naboti wa ku Yezireeli amene anali ndi munda wamphesa ku Yezireeli, pafupi ndi nyumba ya mfumu Ahabu, mfumu ya ku Samariya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zitatha izi, kunaoneka zotere: Naboti wa ku Yezreeli anali ndi munda wamphesa, unali m'Yezreelimo, m'mbali mwa nyumba ya Ahabu mfumu ya ku Samaria.