1 Kings 21:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ahabu atangomva kuti Naboti wafa, adanyamuka napita ku munda wamphesa wa Naboti Myezireele, nautenga kuti ukhale wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, atamva Ahabu kuti Naboti Myezireele wafa, Ahabu anauka kukatsikira ku munda wamphesa wa Naboti, kuulandira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ahabu atamva kuti Naboti wafa, ananyamuka kukatenga munda wamphesa wa Naboti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, atamva Ahabu kuti Naboti wafa, Ahabu anauka kukatsikira ku munda wamphesa wa Naboti, kuulandira.