1 Kings 21:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Chauta adauza Eliya wa ku Tisibe kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mau a Yehova anadza kwa Eliya wa ku Tisibe, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehova anayankhula ndi Eliya wa ku Tisibe kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mau a Yehova anadza kwa Eliya waku Tisibe, nati,