1 Kings 21:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nyamuka, pita ukakumane ndi Ahabu, mfumu ya ku Israele, amene akukhala ku Samariya. Iyeyu ali ku munda wamphesa wa Naboti. Wapita kumeneko kuti akatenge mundawo kuti ukhale wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyamuka, tsikira kukakomana ndi Ahabu mfumu ya Israele, akhala m'Samariya; taona, ali ku munda wamphesa wa Naboti kumene anatsikira kukaulandira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nyamuka, pita ukakumane ndi Ahabu, mfumu ya Israeli amene amalamulira ku Samariya. Pano ali ku munda wamphesa wa Naboti kumene wapita kuti akatenge mundawo kuti ukhale wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyamuka, tsikira kukakomana ndi Ahabu mfumu ya Israyeli, akhala m'Samariya; taona, ali ku munda wamphesa wa Naboti kumene anatsikira kukaulandira.