1 Kings 21:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Chauta adauza Eliya wa ku Tisibe kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mau a Yehova anadza kwa Eliya wa ku Tisibe, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Yehova anayankhula ndi Eliya wa ku Tisibe kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mau a Yehova anadza kwa Eliya wa ku Tisibe, nati,