1 Kings 21:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yezebele, mkazi wake uja, adabwera kwa iye namufunsa kuti, “Chifukwa chiyani nkhope yanu ikuwoneka yosakondwa, ndipo simukufuna chakudya?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yezebele mkazi wake anadza kwa iye, nati kwa iye, Muchitiranji msunamo, kuti mukana kudya mkate?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yezebeli mkazi wake analowa ndipo anamufunsa kuti, “Chifukwa chiyani mukuoneka achisoni? Chifukwa chiyani simukufuna chakudya?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yezebeli mkazi wace anadza kwa iye, nati kwa iye, Mucitiranji msunamo, kuti mukana kudya mkate?