1 Kings 21:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'makalatamo adalembamo kuti, “Lalikani kuti anthu asale zakudya, ndipo Naboti amuike pa malo aulemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analemba m'akalata, nati, Lalikirani kuti asale kudya, muike Naboti pooneka ndi anthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmakalatamo Yezebeli analemba kuti: “Lengezani kuti anthu asale chakudya ndipo muyike Naboti pa malo aulemu pakati pa anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analemba m'akalata, nati, Lalikirani kuti asale kudya, muike Naboti pooneka ndi anthu;