1 Kings 22:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mfumu ya ku Israele idafunsa Yehosafati kuti. “Suja ndidaakuuzani kuti ameneyu sadzandilosera zabwino, koma zoipa zokha?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mfumu ya Israele inanena ndi Yehosafati, Kodi sindinakuuza kuti uyu sadzanenera za ine zabwino, koma zoipa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu ya ku Israeli inati kwa Yehosafati, “Kodi ine sindinakuwuzeni kuti ameneyu samanenera kanthu kalikonse kabwino ka ine, koma zoyipa zokhazokha?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mfumu ya Israyeli inanena ndi Yehosafati, Kodi sindinakuuza kuti uyu sadzanenera za ine zabwino, koma zoipa?