1 Kings 22:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka chachitatu Yehosafati mfumu ya ku Yuda adakacheza kwa Ahabu, mfumu ya ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kunachitika chaka chachitatu, kuti Yehosafati mfumu ya Yuda anatsikira kwa mfumu ya Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pa chaka chachitatu, Yehosafati mfumu ya ku Yuda anapita kukacheza ndi mfumu ya ku Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kunacitika caka cacitatu, kuti Yehosafati mfumu ya Yuda anatsikira kwa mfumu ya Israyeli.