1 Kings 22:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adati, ‘Kodi ndani amene akanyengerere Ahabu kuti akafe ku Ramoti-Giliyadi?’ Wina ankanena zina, winanso nkumanena zina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Yehova, Adzanyenga Ahabu ndani, kuti akwere nagwe ku Ramoti Giliyadi? Ndipo anati wina mwakuti, wina mwakuti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehova anati, ‘Kodi ndani amene akamukope Ahabu kuti akathire nkhondo Ramoti Giliyadi, nʼkukafera komweko?’ ” “Wina anapereka maganizo ena ndipo winanso maganizo ena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Yehova, Adzanyenga Ahabu ndani, kuti akwere nagwe ku Ramoti Gileadi? Ndipo anati wina mwakuti, wina mwakuti.