1 Kings 22:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mzimu wina udadzaima pamaso pa Chauta nunena kuti, ‘Ndikamnyengerera ndine.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mzimu wina unatuluka, nuima pamaso pa Yehova, nuti, Ndidzamnyenga ndine. Nati Yehova kwa iye, Motani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Potsirizira, mzimu wina unabwera ndi kuyima pamaso pa Yehova ndipo unati, ‘Ine ndidzamukopa.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mzimu wina unaturuka, nuima pamaso pa Yehova, nuti, Ndidzamnyenga ndine. Nati Yehova kwa iye, Motani?