1 Kings 22:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsonotu Chauta waika bodza m'kamwa mwa aneneri anu onseŵa, ndiye kuti Iye yemwe waneneratu kuti mukaona tsoka.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano taonani, Yehova waika mzimu wonama m'kamwa mwa aneneri anu onse awa, ndipo Yehova ananena choipa cha inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndipo tsopano taonani, Yehova wayika mzimu wabodza mʼkamwa mwa aneneri anu onsewa. Yehova waneneratu kuti mukaona mavuto.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano taonani, Yehova waika mzimu wonama m'kamwa mwa aneneri anu onse awa, ndipo Yehova ananena coipa ca inu.