1 Kings 22:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mikaya adayankha kuti, “Udzadziŵa pa tsiku limene uzikaloŵa m'chipinda china ndi china cham'kati kuti ukabisale.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mikaya nati, Taona, udzapenya tsiku lolowa iwe m'chipinda cha pakati kubisala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikaya anayankha kuti, “Udzaona pa tsiku limene uzikalowa mʼchipinda chamʼkati kuti ukabisale.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mikaya nati, Taona, udzapenya tsiku lolowa iwe m'cipinda ca pakati kubisala.