1 Kings 22:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukaŵauze mau angaŵa akuti, ‘Munthu uyu muikeni m'ndende ndipo muzimpatsa chakudya pang'ono ndi madzi pang'ono mpaka nditabwerera mwamtendere.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo muziti, Itero mfumu, Khazikani uyu m'kaidi, mumdyetse chakudya cha nsautso, ndi madzi a nsautso, mpaka ndikabwera ndi mtendere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo mukanene kuti, ‘Chimene mfumu ikunena ndi ichi; Muyikeni mʼndende munthu uyu ndipo musamupatse chakudya china koma buledi ndi madzi pangʼono mpaka nditabwerera mwamtendere.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo muziti, Itero mfumu, Khazikani uyu m'kaidi, mumdyetse cakudya ca nsautso, ndi madzi a nsautso, mpaka ndikabwera ndi mtendere.