1 Kings 22:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene dzuŵa linkaloŵa kudamveka mfuu wa ankhondo kuti, “Aliyense apite ku mzinda wakwao, aliyense apite ku dziko lakwao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfuu unafikira khamu lonse la nkhondo polowa dzuwa, ndi kuti, Yense kumudzi kwao, ndi yense ku dziko la kwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene dzuwa linkalowa, kunamveka mfuwu wa nkhondo kuti, “Munthu aliyense apite ku mzinda wa kwawo, aliyense apite ku dziko la kwawo!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfuu unafikira khamu lonse la nkhondo polowa dzuwa, ndi kuti, Yense kumudzi kwao, ndi yense ku dziko la kwao.