1 Kings 22:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero mfumu ija idafa, ndipo anthu adapita nayo ku Samariya, nakaiika m'manda kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo inafa mfumu, naifikitsa ku Samariya, naika mfumu m'Samariya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mfumu ija inafa, nabwera nayo ku Samariya, ndipo anayika mʼmanda kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo inafa mfumu, naifikitsa ku Samaria, naika mfumu m'Samaria.