1 Kings 22:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yehosafati, mwana wa Asa, adayamba kulamulira ku Yuda pa chaka chachinai cha ufumu wa Ahabu, mfumu ya ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehosafati mwana wa Asa anayamba kukhala mfumu ya Yuda chaka chachinai cha Ahabu mfumu ya Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehosafati, mwana wa Asa anakhala mfumu ya ku Yuda chaka chachinayi cha Ahabu mfumu ya ku Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehosafati mwana wa Asa anayamba kukhala mfumu ya Yuda caka cacinai ca Ahabu mfumu ya Israyeli.