1 Kings 22:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Masiku amenewo ku Edomu kunalibe mfumu, koma kunali nduna yaikulu chabe yoikidwa ndi mfumu ya ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'Edomu munalibe mfumu, koma kazembe wa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi imeneyo kunalibe mfumu ku Edomu, amene ankalamulira anali munthu woyikidwa ndi mfumu ya ku Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'Edomu munalibe mfumu, koma kazembe wa mfumu.