1 Kings 22:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yehosafati adauza Ahabu kuti, “Poyamba upemphe nzeru kwa Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehosafati ananena ndi mfumu ya Israele, Funsira ku mau a Yehova lero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehosafati anawuzanso mfumu ya ku Israeli kuti, “Poyamba mupemphe nzeru kwa Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehosafati ananena ndi mfumu ya Israyeli, Fuusira ku mau a Yehova lero.