1 Kings 22:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yehosafati adafunsa kuti, “Kodi pano palibe mneneri wina wa Chauta woti timpempheko nzeru?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehosafati anati, Kodi pano palibe mneneri wina wa Yehova, kuti tifunsire kwa iye?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehosafati anafunsa kuti, “Kodi kuno kulibenso mneneri wina wa Yehova kumene ife tingakafunsireko nzeru?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehosafati anati, Kodi pano palibe mneneri wina wa Yehova, kuti tifunsire kwa iye?