1 Kings 22:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Ahabu adaitana imodzi mwa nduna zake nkuiwuza kuti, “Takaitanani Mikaya, mwana wa Imila, abwere kuno msanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono mfumu ya Israele anaitana mdindo, nati, Kamtenge msanga Mikaya mwana wa Imila.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho mfumu ya Israeli inayitana mmodzi mwa atumiki ake ndipo inati, “Kayitane Mikaya mwana wa Imula msangamsanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono mfumu ya Israyeli anaitana mdindo, nati, Kamtenge msanga Mikaya mwana wa Yimla.