1 Kings 3:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina akazi aŵiri adama adadza kwa Solomoni naimirira pamaso pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo analowa kwa mfumu akazi awiri, ndiwo adama, naima pamaso pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi ina amayi awiri adama anabwera kwa mfumu ndipo anayima pamaso pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo analowa kwa mfumu akazi awiri, ndiwo adama, naima pamaso pace.