1 Kings 3:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mwana wa mnzangayu adafa usiku, chifukwa adaamugonera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwana wa mnzangayu anamwalira usiku, pokhala iyeyu anamgonera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nthawi ya usiku mwana wa mnzangayu anafa chifukwa anamugonera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwana wa mnzangayu anamwalira usiku, pokhala iyeyu anamgonera.