1 Kings 3:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye mfumuyo idati, “Patseni lupanga.” Adabwera nalo lupanga kwa mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Niti mfumu, Kanditengereni chimpeni. Ndipo iwo anabwera ndi chimpeni kwa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mfumu inati, “Patseni lupanga.” Ndipo anabwera nalo lupanga kwa mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Niti mfumu, Kanaitengereni cimpeni. Ndipo iwo anabwera ndi cimpeni kwa mfumu.