1 Kings 3:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu idagamula kuti, “Mduleni pakati mwana wamoyoyu, aliyense mwa azimai aŵiriŵa mumpatse chigawo chimodzi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu niti, Dula pakati mwana wamoyoyu, nupatse mmodzi chipinjiri, ndi wina chipinjiri chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mfumu inagamula kuti, “Muduleni pakati mwana wamoyoyu ndipo wina mumupatse gawo limodzi, gawo linalo mumupatse winayo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu niti, Dula pakati mwana wamoyoyu, nupatse mmodzi cipinjiri, ndi wina cipinjiri cace.