1 Kings 3:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu idayankha kuti, “Perekani mwana wamoyoyu kwa mai woyamba uja, musamuphe ai. Ameneyu ndiye mai wake wa mwanayu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mfumu inayankha, niti, Mumpatse wachifundoyo mwana wamoyo, osamupha konse, uyo ndiye amake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho mfumu inagamula kuti, “Perekani mwana wamoyoyu kwa mayi woyambayu. Musamuphe, iyeyu ndiye mayi wake wa mwanayu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mfumu inayankha, niti, Mumpatse wacifundoyo mwana wamoyo, osamupha konse, uyo ndiye amace.