1 Kings 3:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ine mtumiki wanu ndikukhala pakati pa anthu amene mudaŵasankha, mtundu waukulu, anthu ake ochuluka, oti nkosatheka kuŵaŵerenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kapolo wanu ndili pakati pa anthu anu amene Inu munawasankha, anthu ambirimbiri osawerengeka, kapena kulembeka m'unyinji wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtumiki wanu ali pakati pa anthu amene munawasankha, mtundu waukulu, anthu ochuluka kwambiri osatheka kuwawerenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kapolo wanu ndiri pakati pa anthu anu amene Inu munawasankha, anthu ambirimbiri osawerengeka, kapena kulembeka m'unyinji wao.