1 Kings 4:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Benabidanabu ankayang'anira dziko lonse la mapiri la Dori. Iyeyo anali atakwatira Tafati mwana wa Solomoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Benabinadabu ku mtunda wa Dori, mkazi wake ndiye Tafati mwana wa Solomoni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Beni-Abinadabu, woyangʼanira Nafoti Dori (iye anakwatira Tafati mwana wa Solomoni);
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Benabinadabu ku mtunda wa Dori, mkazi wace ndiye Tafati mwana wa Solomo;