1 Kings 4:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Baana mwana wa Ahiludi ankayang'anira ku Tanaki, Megido ndi ku Beteseani konse, pafupi ndi Zaretani kunsi kwake kwa Yezireele, ndiponso kuyambira ku Beteseani mpaka ku Abele-Mehola kukafika mpaka ku Yokomeamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Baana mwana wa Ahiludi ku Taanaki ndi Megido ndi Beteseani konse, ali pafupi ndi Zaretani kunsi kwa Yezireele, kuyambira ku Beteseani kufikira ku Abele-Mehola, kufikiranso kundunji ku Yokomeamu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Baana mwana wa Ahiludi, anali woyangʼanira Taanaki ndi Megido, ndi ku Beti Sani konse, kufupi ndi ku Zaretani kumunsi kwa Yezireeli, kuyambira ku Beti-Seani mpaka ku Abeli-Mehola kukafika mpaka ku Yokineamu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Baana mwana wa Ahiludi ku Tanaki ndi Megido ndi Betseani konse, ali pafupi ndi Zaratana kunsi kwa Yezreeli, kuyambira ku Betseani kufikira ku Abelimehola, kufikiranso kundunji ku Yokineamu;