1 Kings 4:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abinadabu mwana wa Ido ankayang'anira ku Mahanaimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ahinadabu mwana wa Ido ku Mahanaimu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ahinadabu mwana wa Ido, anali woyangʼanira Mahanaimu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Abinadabu mwana wa Ido ku Nahanaimu;