1 Kings 4:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ahimaazi ankayang'anira ku Nafutali. Iyeyu adaakwatira Basemati mwana wa Solomoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ahimaazi ku Nafutali, iyeyu adakwatira Basemati mwana wa Solomoni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ahimaazi anali woyangʼanira Nafutali (iyeyu anakwatira Basemati mwana wa Solomoni);
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ahimazi ku Nafitali, iyeyu adakwatira Basemati mwana wa Solomo;