1 Kings 4:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Baana, mwana wa Husai ankayang'anira ku Asere ndi ku Bealoti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Baana mwana wa Husai ku Asere ndi ku Bealoti;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Baana mwana wa Husai, anali woyangʼanira Aseri ndi Bealoti;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Baana mwana wa Husayi ku Aseri ndi ku Aloti;