1 Kings 4:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gebere, mwana wa Uri, ankayang'anira ku dziko la Giliyadi kuphatikizapo dziko limene lidaali la Sihoni mfumu ya Aamori, ndiponso la Ogi mfumu ya ku Basani. Panalinso nduna yaikulu imodzi yoyang'anira dziko lonse la Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Gebere mwana wa Uri ku dziko la Giliyadi, dziko la Sihoni mfumu ya Aamori, ndi la Ogi mfumu ya Basani; munalibe kapitao wina m'deramo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Geberi mwana wa Uri, anali woyangʼanira Giliyadi (dziko la Sihoni mfumu ya Aamori ndi dziko la Ogi mfumu ya Basani). Iye ankayangʼanira chigawo chonsechi yekha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Geberi mwana wa Uri ku dziko la Gileadi, dziko la Sihoni mfumu ya Aamori, ndi la Ogi mfumu ya Basani; munalibe kapitao wina m'deramo.