1 Kings 4:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo nduna zake zikuluzikulu zinali izi: Azariya mwana wa Zadoki anali wansembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akulu a mfumu ndi awa: Azariya mwana wa Zadoki anali wansembe,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nduna zake zikuluzikulu zinali izi: Azariya mwana wa Zadoki anali wansembe;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akuru a mfumu ndi awa: Azariya mwana wa Zadoki anali nduna,