1 Kings 4:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chakudya chofunika ku nyumba ya mfumu pa tsiku limodzi chinkakwanira madengu 150 a ufa wosalala ndi madengu 300 a mgaiwa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zakudya za Solomoni zofikira tsiku limodzi zinali miyeso makumi atatu ya ufa wosalala, ndi miyeso makumi asanu ndi limodzi ya ufa wamankhupete,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chakudya cha tsiku ndi tsiku cha Solomoni chinali madengu 150 a ufa wosalala ndi madengu 300 a mgayiwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zakudya za Solomo zofikira tsiku limodzi zinalr miyeso makumi atatu ya ufa wosalala, ndi miyeso makumi asanu ndi limodzi ya ufa wamankhupete,