1 Kings 4:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankaphunzitsa za mitengo, kuyambira mkungudza wa ku Lebanoni mpaka kachitsamba ka hisope komera pa khoma. Ankaphunzitsanso za nyama, mbalame, zinthu zokwawa pansi ndiponso za nsomba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakamba za mitengo, kuyambira mkungudza uli ku Lebanoni kufikira hisope wophuka pakhoma; anakambanso za nyama ndi mbalame ndi zinthu zokwawa pansi ndi za nsomba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ankaphunzitsa za mitengo, kuyambira mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni mpaka kachitsamba ka hisope khomera pa khoma. Iye ankaphunzitsanso za nyama ndi mbalame, zinthu zokwawa pansi ndiponso za nsomba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakamba za mitengo, kuyambira mkungudza uli ku Lebano kufikira hisopi wophuka pakhoma; anakambanso za nyama ndi mbalame ndi zinthu zokwawa pansi ndi za nsomba.