1 Kings 4:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Azariya mwana wa Natani ankayang'anira nduna zam'zigawo. Zabudi mwana wa Natani anali wansembe ndi mlangizi wapadera wa mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Azariya mwana wa Natani anayang'anira akapitao, ndipo Zabudi mwana wa Natani anali wansembe ndi nduna yopangira mfumu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Azariya mwana wa Natani, anali woyangʼanira nduna za mʼzigawo; Zabudi mwana wa Natani, anali wansembe ndi bwenzi la mfumu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Azariya mwana wa Natani anayang'anira akapitao, ndi Zabudi mwana wa Natani anali nduna yopangira mfumu,