1 Kings 5:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Analinso ndi akapitao 3,300 amene ankayang'anira anthu ogwira ntchito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
osawerenga akapitao a Solomoni akuyang'anira ntchito, ndiwo zikwi zitatu mphambu mazana atatu, amenewo analamulira anthu aja akugwira ntchito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi akapitawo 33,000 amene ankayangʼanira ntchitoyi ndiponso anthu ogwira ntchito zina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
osawerenga akapitao a Solomo akuyang'anira nchito, ndiwo zikwi zitatu mphambu mazana atatu, amenewo analamulira anthu aja akugwira nchito.