1 Kings 6:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kerubi winayo msinkhu wake unalinso mamita anai ndi theka. Akerubi aŵiri onsewo anali a misinkhu yofanana ndi a mapangidwe ofanananso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kerubi winayo msinkhu wake unali mikono khumi; akerubi onse awiri anafanana muyeso wao ndi msinkhu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kerubi wachiwiriyo msinkhu wake unalinso mamita anayi ndi theka, pakuti akerubi awiriwo anali a misinkhu yofanana ndi a mapangidwe ofanana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kerubi winayo msinkhu wace unali mikono khumi; akerubi onse awiri anafanana muyeso wao ndi msinkhu wao.