1 Kings 6:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kerubi mmodzi msinkhu wake unali mamita anai ndi theka, kerubi winayo analinso chimodzimodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Msinkhu wa kerubi mmodzi unali mikono khumi, ndi wa kerubi wina momwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Msinkhu wa kerubi aliyense unali mamita anayi ndi theka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Msinkhu wa kerubi mmodzi unali mikono khumi, ndi wa kerubi wina momwemo.