1 Kings 6:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adayalanso golide pansi m'Nyumbamo m'zipinda zam'kati ndi zakunja zomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakuta ndi golide pansi pake pa nyumba m'katimo ndi kunja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anayala golide pansi mu Nyumbamo mʼzipinda zamʼkati ndi zakunja zomwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakuta ndi golidi pansi pace pa nyumba m'katimo ndi kunja.