1 Kings 6:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maziko a Nyumba ya Chauta adamangidwa pa chaka chachinai, mwezi wa Zivi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maziko ake a nyumba ya Yehova anaikidwa m'chaka chachinai m'mwezi wa Zivi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maziko a Nyumba ya Yehova anamangidwa pa chaka chachinayi, mwezi wa Zivi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maziko ace a nyumba ya Mulungu anaikidwa m'caka cacinai m'mwezi wa Zivi.