1 Kings 6:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaika mawindo amene mafuremu ake anali oloŵa m'kati mwa makoma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'nyumbamo anamanga mazenera a sefa wokhazikika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanga mazenera amene maferemu ake anali olowa mʼkati mwa makoma a Nyumbayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'nvumbamo anamanga mazenera a made okhazikika.