1 Kings 6:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamanganso zipinda zosanjikizana pafupi ndi khoma la Nyumba, kuzungulira makoma a Nyumba yaikuluyo ndi a malo opatulika a m'kati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamanga zipinda zosanjikizana zogundana ndi khoma, kuzungulira makoma a nyumba ya Kachisi, ndi chipinda chamkati; namanga zipinda zozinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmbali mwa makoma a Nyumba yayikulu ndi chipinda chopatulika chamʼkati, anamanga zipinda zosanjikizana, mozungulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamanga zipinda zosanjikizana zogundana ndi khoma, kuzungulira makoma a nyumba ya Kacisi, ndi monenera momwemo; namanga zipinda zozinga,