1 Kings 7:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Solomoni adatha zaka khumi ndi zitatu akumanga nyumba yake yachifumu, ndipo adaimariza nyumba yonseyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma nyumba ya iye yekha Solomoni anaimanga zaka khumi mphambu zitatu, natsiriza nyumba yake yonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Solomoni anamanga nyumba yake yaufumu kwa zaka 13.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma nyumba ya iye yekha Solomo anaimanga zaka khumi mphambu zitatu, natsiriza nyumba yace yonse.