1 Kings 7:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mazikowo adamangidwa ndi miyala yabwino kwambiri, yaikulu bwino, kutalika kwake inali mamita atatu ndi theka, ina mamita anai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo maziko ake anali a miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yaikulu, miyala ya mikono khumi, ndi miyala ya mikono isanu ndi itatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maziko ake anali a miyala yabwino kwambiri, kutalika kwa miyala ina kunali mamita atatu ndi theka, inanso mamita anayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo maziko ace anali a miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yaikulu, miyala ya mikono khumi, ndi miyala ya mikono isanu ndi itatu.